Zamanja Is A Malawian local expert directory
Verified Phone and Computer technicians, plumbers, electricians, mechanics, beauticians near you. Rated by people who've actually hired them.
Filter through experts to find who you need for your specific problem.
Questions
Zamanja is a local directory that connects you with verified plumbers, electricians, mechanics, carpenters, IT technicians and other skilled experts in your area.
Zamanja ndi malo apa intaneti amene amathandiza anthu kupeza akatswiri antchito monga ma plumber, amagetsi, amakina, akalipentala, aukadaulo okonza ma phone ma computer, ndi ena m'dera lanu.
You can go on the find link on the menu or browse through filter experts.
Mukuyenera kutobwanya mawu alembedwa kuti Find kapena Filter Experts.
We review every expert profile before it goes live, and we display customer ratings so you can see how others rate their work before you reach out.
Timaunika mbiri iliyonse ya katswiri asanaonetsedwe pa webusaiti, ndipo timawonetsa maonekedwe a makasitomala kuti mudziwe momwe ena amaonera ntchito yawo musanapemphe thandizo.
Searching for and contacting experts is completely free for customers. Service providers can list a basic profile for free, with optional paid features to help them stand out.
Kufufuza ndi kulumikizana ndi akatswiri ndi kwaulere kwanthunthu kwa makasitomala. Anthu ogwira ntchito za ukadawulo, ndi oleledwa kupanga ma account kwa ulere popanda kulipira ndalama ina ili yonse. Koma palinso ma plan ena olipira amene angawathandize kupeza ma customer mwachangu.
Once you find a profile that fits what you need, you can reach out directly through the contact details or message option on their page.
Mukhoza kulumikizana ndi akadawulo kwa ulere kudzera ma nambala awo a phone amene amasiya pama tsamba awo.
You can create a free account, upload your details and the services you offer. You will be listed immediately.
Mutha kupanga account kwa ulere, kenako kulemba zomwe mumapanga ku account kwanu. Mukatero, mupezeka ntchito yanu ipezeka pa Zamanja
Zamanja is found everywhere in Malawi where experts have listed their businesses.
Zamanja ikupezeka pali ponse ku Malawi pamene madolo amudela lanu apanga zokhala ndi malo pa Zamanja pano.
You can leave a review at the expert's page or call of WhatsApp us directly on +265883292173 or you can email us on zamanja455@gmail.com.
Mukhoza kulemba zaku nkhosi zanu mmene simunakhutislilidwe ndi ntchito munalanda pa tsamba la dolo yo, kapena mutha kutiwuza ife (+265883292173/info@zamanja.org).